Ulosi wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa dzinja la 2025-2026 umene ukuunikira ammene mvula igwere mmaboma onse a Malawi. Ulosiwu ukupereka upangili omwe uthandize onse ogwilitsa ntchito ulosiwu kukonzekera ziopysezo zonse zobwera ndi nyengo ya dzinja limeneli
Browse Product Updates
Boma la Nkhotakota likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuposera apo munyengo ya dzinja ya 2025/2026.
Boma la Ntcheu likuyembekezereka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena mlingo ochepera okhazikika mu nyengo ya mvula ya 2025/2026.
Boma la Phalombe likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena woposera apo mu nyengo ya mvula ya 2025/2026.
Boma la Chikwawa likuyembekeza kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena yoposera apo mu nyengo ya dzinja la 2025/2026
Boma la Salima likuyembekezeka kulandira mvula mlingo wokhazikika kapena kuposera apo.
Boma la Chitipa likuyembekezera kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuchepera apo mu dzinja la 2025/2026