Ulosi wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa dzinja la 2025-2026 umene ukuunikira ammene mvula igwere mmaboma onse a Malawi. Ulosiwu ukupereka upangili omwe uthandize onse ogwilitsa ntchito ulosiwu kukonzekera ziopysezo zonse zobwera ndi nyengo ya dzinja limeneli
Browse Product Updates
Filter by Year
Filter by Month
Showing 29 results
Ulosi wa Lilongwe wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Lilongwe likuyembekeza kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena yoposerapo mu nyengo ya dzinja la 2025/2026
Ulosi wa Machinga wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Machinga likuyembekezeka kudzalandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuchepela apo mu dzinjali.
Ulosi wa Mangochi wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Mangochi likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuposera apo
Ulosi wa Nchinji wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Mchinji likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena mlingo woposera wokhazikika
Ulosi wa Mulanje wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Mulanje likuyembekezeka kulandira mvula ya mulingo wokhadzikika mu dzinja la 2025/2026.
Ulosi wa Dowa wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Dowa likuyembekezera kudzalandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuchepera apo mu dzinjali kuyambira mu nyengo ya dzinja ya 2025/2026