Ulosi wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa dzinja la 2025-2026 umene ukuunikira ammene mvula igwere mmaboma onse a Malawi. Ulosiwu ukupereka upangili omwe uthandize onse ogwilitsa ntchito ulosiwu kukonzekera ziopysezo zonse zobwera ndi nyengo ya dzinja limeneli
Browse Product Updates
Boma la Mchinji likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena mlingo woposera wokhazikika
Boma la Mulanje likuyembekezeka kulandira mvula ya mulingo wokhadzikika mu dzinja la 2025/2026.
Boma la Mwanza likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo okhazikika mu nyengo ya dzinja ya mchaka cha 2025/2026
Boma la Mzimba likuyembekezereka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena mlingo woposera wokhazikika mu nyengo ya mvula ya 2025/2026
Boma la Nkhatabay likuyembekezera kulandira mvula ya mlingo wokhadzikika kapena kuposerapo ngakhale pali kuthekera kwakukulu koti mvula yochepera mlingo wokhad…
Boma la Mangochi likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuposera apo