Weekly Weather Update
The Malawi Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS) offers a weekly weather forecast, providing citizens with reliable and up-to-date weather predictions. This essential service helps in planning agricultural, economic, and daily activities, enhancing resilience against weather-related challenges.
Browse Product Updates
Filter by Year
Filter by Month
Showing 30 results
Nyengo msabata ikubwerayi 28 Oct - 3 Nov 2024
Tiyembekezere nyengo ya mvula ya mabingu ndi mphepo ya mkuntho mmadera ena. Nyengoyi idzayamba Lolemba m’madera am’zigawo za pakati ndi kumpoto ndipo idzafalikira m’madera am’chigawo cha kum’mwera pofika Lachiwiri pa 29 October 2024. Izi zikhala …
Weekly Weather Update 28 Oct - 3 Nov 2024
The upcoming week is expected to be generally wet across many areas. Rain, lightning, and potentially damaging winds will initially affect parts of the central and northern regions on Monday, spreading to southern areas by …
Nyengo msabata ikubwerayi 21- 27 Oct 2024
Kukhala kwa nyengo yopanda mvula m'madera ambiri. Koma pali kuthekera kwa mvula yowaza yamabingu m’madera ochepa am’chigawo cha kumpoto ndi okwera am’chigawo cha ku m’mwera.
Weekly Weather Update 21 - 27 Oct 2024
During the upcoming week, until Sunday 27th October, predominantly dry weather with mostly sunny and hot conditions are expected . However, thundery showers are possible in few parts of the northern areas and a few …
Weekly Weather Update 14 - 20 Oct 2024
⛅⛅Expect partly cloudy and hot conditions to be dominant over many areas during this week.
🌧️🌧️However between Tuesday the 15th and Thursday the 17th October 2024 expect windy and cloudy conditions with localized thunderstorms and …
Nyengo msabata ikubwerayi 14- 20 Oct 2024
Tiyembekezere nyengo yamitambo yapatali patali komanso yotentha msabatayi.
🌧️Koma pakati pa lachiwiri masana pa 15 October 2024 mpaka lachinayi pa 17 October 2024, tiyembekezere nyengo ya mphepo, yamitambo komanso mvula ya mabingu m’madera ena.
⚠️🌊Mphepo …