Ulosi wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa dzinja la 2025-2026 umene ukuunikira ammene mvula igwere mmaboma onse a Malawi. Ulosiwu ukupereka upangili omwe uthandize onse ogwilitsa ntchito ulosiwu kukonzekera ziopysezo zonse zobwera ndi nyengo ya dzinja limeneli
Browse Product Updates
Filter by Year
Filter by Month
Showing 29 results
Ulosi wa Dedza wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Dedza likuyembekezereka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena mlingo woposera wokhazikika mu nyengo ya mvula ya 2025/2026
Ulosi wa Mwanza wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Mwanza likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo okhazikika mu nyengo ya dzinja ya mchaka cha 2025/2026
Ulosi wa Karonga wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Karonga likuyembekezera kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuposera apo mu nyengo ya mvula ya 2025/2026.
Ulosi wa Kasungu wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Kasungu likuyembekezera kulandira mvula ya mlingo wokhazikika mu nyengo ya Dzinja ya 2025/2026.
Ulosi wa Likoma wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Likoma tiyembekezere mvula ya mlingo okhazikika mu dzinja la 2025/2026
Ulosi wa Chikwawa wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Chikwawa likuyembekeza kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena yoposera apo mu nyengo ya dzinja la 2025/2026