Ulosi wa Dzinja la 2025-2026

Ulosi wa dzinja la 2025-2026 umene ukuunikira ammene mvula igwere mmaboma onse a Malawi. Ulosiwu ukupereka upangili omwe uthandize onse ogwilitsa ntchito ulosiwu kukonzekera ziopysezo zonse zobwera ndi nyengo ya dzinja limeneli

Ulosi wa Dzinja la 2025-2026

Browse Product Updates

Year
Month
Showing 29 results
Ulosi wa Rumphi wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa Rumphi wa Dzinja la 2025-2026

Madera ambiri m’boma Rumphi akuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo okhazikika kapena kuchepera apo mu dzinja la 2025/2026.

Ulosi wa Zomba wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa Zomba wa Dzinja la 2025-2026

Boma la Zomba likuyembekezereka kulandira mvula pa mlingo wokhazikika komaso wocheperako pa mlingo wokhazikika miyezi ina.

Ulosi wa Balaka wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa Balaka wa Dzinja la 2025-2026

Boma la Balaka likuyembekeza kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena wocheperapo mu nyengo ya dzinja ya 2025/2026.

Ulosi wa Neno wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa Neno wa Dzinja la 2025-2026

Boma la Neno likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika mu nyengo ya dzinja la 2025/2026

Ulosi wa Nsanje wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa Nsanje wa Dzinja la 2025-2026

Boma la Nsanje likuyembekezereka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuposera mu nyengo ya mvula ya 2025/2026.

Ulosi wa Mangochi wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa Mangochi wa Dzinja la 2025-2026

Boma la Mangochi likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuposera apo