Ulosi wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa dzinja la 2025-2026 umene ukuunikira ammene mvula igwere mmaboma onse a Malawi. Ulosiwu ukupereka upangili omwe uthandize onse ogwilitsa ntchito ulosiwu kukonzekera ziopysezo zonse zobwera ndi nyengo ya dzinja limeneli

Browse Product Updates
Filter by Year
Filter by Month
Showing 28 results

Ulosi wa Kasungu wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Kasungu likuyembekezera kulandira mvula ya mlingo wokhazikika mu nyengo ya Dzinja ya 2025/2026.

Ulosi wa Likoma wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Likoma tiyembekezere mvula ya mlingo okhazikika mu dzinja la 2025/2026

Ulosi wa Lilongwe wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Lilongwe likuyembekeza kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena yoposerapo mu nyengo ya dzinja la 2025/2026

Ulosi wa Machinga wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Machinga likuyembekezeka kudzalandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuchepela apo mu dzinjali.