Ulosi wa Dzinja la 2025-2026
Ulosi wa dzinja la 2025-2026 umene ukuunikira ammene mvula igwere mmaboma onse a Malawi. Ulosiwu ukupereka upangili omwe uthandize onse ogwilitsa ntchito ulosiwu kukonzekera ziopysezo zonse zobwera ndi nyengo ya dzinja limeneli
Browse Product Updates
Boma la Mzimba likuyembekezereka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena mlingo woposera wokhazikika mu nyengo ya mvula ya 2025/2026
Boma la Neno likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika mu nyengo ya dzinja la 2025/2026
Boma la Nkhatabay likuyembekezera kulandira mvula ya mlingo wokhadzikika kapena kuposerapo ngakhale pali kuthekera kwakukulu koti mvula yochepera mlingo wokhad…
Boma la Nkhotakota likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuposera apo munyengo ya dzinja ya 2025/2026.
Boma la Ntchisi likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuposera apo mudzinjali
Madera ambiri m’boma Rumphi akuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo okhazikika kapena kuchepera apo mu dzinja la 2025/2026.