Salima District Downscaled Seasonal Forecast 2026-2027

Bulletin

Madera ambiri a Boma la Salima akuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuposera apo miyezi ya October mpaka December, koma mvula yochepa miyezi ya January ndi February.

Salima District is expected to receive normal to above-normal rainfall during October to December with higher chances of normal to below-normal rainfall during January and February.