CAP Alert · Actual

Mphepo ya Mwera pa Nyanja

Expired: Strong Mwera winds
Moderate severity
Urgency Expected
Severity Moderate
Certainty Likely
Category Met
Language en
Time period
  • Issued 14 Mar 2025 12:06
  • Effective 14 Mar 2025 13:00
  • Onset 16 Mar 2025 12:01
  • Expires 18 Mar 2025 12:01
Severity
Extreme
Severe
Moderate
Minor

Mphepo ya Mwera pa Nyanja

Area

Lake Malawi, Lake Chilwa, Lake Malombe

Event description

Mphepo ya mphamvu ya Mwera ikuyembekezeka kuomba pa nyanja zathu kuphatikizapo pa nyanja ya Malawi, ya Chilwa ndi ya Malombe.

Instructions

1. Tipewe kugwiritsa ntchito ngalawa zing'onozing'ono. 2. Tipewe kusambira panthawiyi 3. Tisalole ana kusewera pafupi ndi nyanja