Expired: Mwera winds
Moderate severity
Urgency Expected
Severity Moderate
Certainty Likely
Category Met
Language en
Time period
  • Issued 17 Apr 2025 16:09
  • Effective 17 Apr 2025 17:00
  • Onset 17 Apr 2025 22:00
  • Expires 21 Apr 2025 17:00
Severity
Extreme
Severe
Moderate
Minor

Mphepo ya Mwera pa Nyanja

Area

Nyanja ya Malawi, Nyanja ya Chilwa

Event description

Mphepo ya mphamvu ya Mwera ya liwiro la 40km/h ikuyembekezeka kuomba pa nyanja zathu kuphatikizapo pa nyanja ya Malawi, ya Chilwa ndi ya Malombe kuyambira mawa ,Lachinayi usiku pa 17 April mpaka Lamulungu pa 20 April 2025. Mphepoyi ikuyembekezeka kuchititsa mafunde owopsa otalika mita imodzi (1 metre).

Instructions

1. Tipewe kugwiritsa ntchito ngalawa zing'onozing'ono. 2. Tipewe kusambira panthawiyi. 3. Tisalole ana kusewera pafupi ndi nyanja