Expired: Mwera winds
Moderate severity
Urgency Expected
Severity Moderate
Certainty Likely
Category Met
Language en
Time period
  • Issued 28 Apr 2025 09:56
  • Effective 28 Apr 2025 10:00
  • Onset 03 May 2025 20:00
  • Expires 07 May 2025 18:00
Severity
Extreme
Severe
Moderate
Minor

Mphepo ya Mwera pa Nyanja

Area

Nyanja ya Malawi, Nyanja ya Chilwa

Event description

Mphepo ya mphamvu ya Mwera ya liwiro la 40km/h ikuyembekezeka kuomba pa nyanja zathu kuphatikizapo pa nyanja ya Malawi, ya Chilwa ndi ya Malombe kuyambira Loweruka usiku pa 3 May 2025 mpaka Lachitatu pa 7 May 2025. Mphepoyi ikuyembekezeka kudzachititsa mafunde owopsa otalika mita imodzi (1 metre).

Instructions

1. Tipewe kugwiritsa ntchito ngalawa zing'onozing'ono. 2. Tipewe kusambira panthawiyi. 3. Tisalole ana kusewera pafupi ndi nyanja