CAP Alert · Actual
Mphepo ya Mwera pa Nyanja
Mphepo ya Mwera pa Nyanja
Area
Nyanja ya Malawi, Nyanja ya Chilwa, Nyanja ya Malombe
Event description
Mphepo ya mphamvu ya Mwera ya liwiro la 36km/h ikuyembekezeka kuomba pa nyanja zathu kuphatikizapo pa nyanja ya Malawi, ya Chilwa ndi ya Malombe kuyambira mawa ,Lachinayi pa 3 April mpaka Lamulungu pa 6 April 2025. Mphepoyi ikuyembekezeka kuchititsa mafunde owopsa otalika mita imodzi (1 metre).
Instructions
1. Tipewe kugwiritsa ntchito ngalawa zing'onozing'ono. 2. Tipewe kusambira panthawiyi. 3. Tisalole ana kusewera pafupi ndi nyanja