CAP Alert · Actual
Madzi Osefukira Mwadzidzidzi Kumpoto Kwa Malawi
Madzi Osefukira Mwadzidzidzi Kumpoto Kwa Malawi
Flood prone and low lying areas in the North mainly in Karonga, Nkhatabay and Rumphi
Mvula ya mphamvu yomwe ikuyembekezeka kugwa m'madera ena am'chigawo cha kumpoto ingachititse madzi kusefukira mwadzidzidzi makamaka ku Nkhatabay, Karonga ndi ku Rumphi.
1. Tikhale tcheru 2. Tithawire kumtunda pakakhala chiopsezo cha kusefukira kwa madzi mwadzidzidzi 3. Tisaoloke madzi osefukira 4. Tisalole ana kusewera pafupi ndi mitsinje, madamu kapena mungalande zodutsa madzi. 5. Tikonze ndi kusamalira ngalande zodutsamo madzi