CAP Alert · Actual

Madzi Osefukira Mwadzidzidzi ku Nyanja

Expired: Flood
Severe severity
Urgency Future
Severity Severe
Certainty Likely
Category Met
Language en
Time period
  • Issued 17 Apr 2025 16:17
  • Effective 17 Apr 2025 17:00
  • Onset 18 Apr 2025 06:00
  • Expires 20 Apr 2025 14:00
Severity
Extreme
Severe
Moderate
Minor

Madzi Osefukira Mwadzidzidzi M'mbali Mwa Nyanja Ya Malawi

Area

Karonga, Nkhatabay

Event description

Mvula ya mphamvu yomwe ikuyembekezeka kugwa m'madera ena am'chigawo cha kumpoto komanso am'mphepete mwa nyanja ingachititse madzi kusefukira mwadzidzidzi makamaka ku Nkhatabay, Karonga.

Instructions

1. Tikhale tcheru 2. Tithawire kumtunda pakakhala chiopsezo cha kusefukira kwa madzi mwadzidzidzi 3. Tisaoloke madzi osefukira 4. Tisalole ana kusewera pafupi ndi mitsinje, madamu kapena mungalande zodutsa madzi. 5. Tikonze ndi kusamalira ngalande zodutsamo madzi