CAP Alert · Actual
Kuzizira M'madera okwera ndi Apakati
Kuzizira M'madera okwera ndi Apakati
Area
Madera okwera ndi am'chigawo chapakati.
Event description
Tikuyembekezera nyengo yozizira m'madera okwera komanso am'chigawo chapakati kamba ka mphepo yozizira komanso ya chinyontho yochokera kumwera cha kumvuma.
Instructions
1. Tivale za mphepo. 2. Anthu omwe ali ndi vuto la mphumu akuyenera kusamalitsa