Sept. 2, 2026
Ulosi wa Dzinja la 2026 - 2027
M’dzinja la 2026/2027 pali kuchepera kwakukulu kolandira mvula yochepera milingo wokhazikika m’madera ambiri a chigawo chakum’mera ndi chapakati chadziko la Malawi, pamene m’madera ambiri a chigawo chakumpoto akuyembekezeka kulandira mvula yamilingo wokhazikika kapena kupola milingowu.