Nyengo msabata ikubwerayi 4-10 May 2026

Weekly Weather Update

Tiyembekezere nyengo yamitambo yapatalipatali ndi yofunda m’madera ambiri, komanso nyengo yozizira nthawi ya usiku ndi m’mbandakucha kuyambira Lachiwiri pa 5 May mpaka pa 10 May 2026 kamba ka mphepo zomwe zidziomba kuchokera kumvuma. Chifunga chikuyembekeza muzigwa makamaka nthawi m’mbandakucha.