Kuyambira mawa mpaka Lachiwiri pa 28 April 2026, tiyembekezere nyengo ya mitambo yapatalipatali, ya chifunga ndi mvula m’madera ochepa makamaka a mphepete mwanyanja a m’chigawo chakumpoto.