Nyengo msabata ikubwerayi 20-26 April 2026
NYENGO M’SABATA IKUBWERAYI
Kuyambira Lolemba mpaka Lachinayi, tiyembekezere nyengo ya mitambo yapatalipatali ndi mvula m’madera ochepa kwambiri chifukwa cha mphepo zochokera kumvuma.