Nyengo msabata ikubwerayi 13-19 April 2026

Weekly Weather Update

NYENGO M’SABATA IKUBWERAYI

M’sabatayi, tiyembekezere madera ambiri kukhala ndi nyengo ya mitambo yapatali patali ndipo mvula izigwa m’madera ochepa koma ya mphamvu maka m'madera a m’phepete mwa nyanja ya Malawi monga ku NkhataBay, Karonga ndi Nkhotakota kamba ka mphepo zochokera kumvuma.