Nyengo msabata ikubwerayi 10- 16 Feb 2025
Sabatayi ikuyembekezeka kukhala ya mvula m’madera ochuluka kamba ka dera lodzetsa mvula la ITCZ zomwe zikuperekanso chiopsyezo cha madzi osefukira mwadzidzidzi m’madera omwe kumakonda kusefukira madzi.