Ntchisi District Downscaled Seasonal Forecast 2026-2027

Bulletin

Boma la Ntchisi likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuposera apo mu miyezi ya October mpaka December ndipo pali kuthekela kolandila mvula yamlingo okhazikika komanso kuchepela apo mu miyezi ya January ndi February.

Ntchisi District is expected to receive generally normal to above-normal rainfall during October to December while chance of normal to below-normal rainfall in January and February.