Lilongwe District Downscaled Seasonal Forecast 2026-2027

Bulletin

Boma la Lilongwe likuyembekeza kulandira mvula ya mlingo wokhazikika mu miyezi ya October mpaka December, komanso pali kuthekela kolandila mvula ya mlingo wokhazikika Kapena kuchepela apo mu miyezi ya January ndi February.

Lilongwe District is expected to receive normal rainfall from October to December while chance of normal to below-normal rainfall in January and February.