Mvula ya mphamvu kum'mwera
Alert Severity:
Extreme
Severe
Moderate
Minor
Mvula ya mphamvu kum'mwera kwa Malawi
Expired: Rain/Wet Spell
Yellow severity
Language:
en
Category:
Met
Urgency:
Future
Severity:
Moderate
Certainty:
Possible
Time period
-
Issued Tue 25 Feb 2025 08:19
-
Effective: Tue 25 Feb 2025 10:00
-
Expires: Fri 28 Feb 2025 08:21
Area
Chigawo cha kumwera
Event Description
Madera ambiri am'chigawo cha kum'mwera akuyembekezeka kulandira mvula yochuluka yoposa mlingo wa 50 mm pa tsiku (ma ola 24) zomwe zikupereka ziopsezo za: 1. kusefukira kwa madzi mwadzidzidzi. 2. Kugwa kwa nyumba komanso zimbuzi.
Instructions
● Madzi osefukira mwadzidzidzi: Tikhale tcheru ndipo tipewe kuoloka madzi osefukira kapena othamanga kuti titeteze miyoyo yathu.
● Mvula ya Mabingu: Kukamagwa mvula ya mabingu tikuyenera kubisala pamalo otetezeka bwino ndipo tipewe kubisala pansi pa mitengo.
● Chinyezi: Tikhale osamala ndi nyumba kapena zimbuzi zomwe zanyowa kwambiri ndi mvula chifukwa zitha kugwa nthawi ina iliyonse.