Mphepo ya Mwera pa Nyanja
Alert Severity:
Extreme
Severe
Moderate
Minor
Mphepo ya Mwera pa Nyanja
Expired: Mwera winds
Yellow severity
Language:
en
Category:
Met
Urgency:
Expected
Severity:
Moderate
Certainty:
Likely
Time period
-
Issued Wed 02 Apr 2025 09:28
-
Effective: Wed 02 Apr 2025 10:00
-
Onset: Thu 03 Apr 2025 10:00
-
Expires: Sun 06 Apr 2025 12:01
Area
Nyanja ya Malawi, Nyanja ya Chilwa, Nyanja ya Malombe
Event Description
Mphepo ya mphamvu ya Mwera ya liwiro la 36km/h ikuyembekezeka kuomba pa nyanja zathu kuphatikizapo pa nyanja ya Malawi, ya Chilwa ndi ya Malombe kuyambira mawa ,Lachinayi pa 3 April mpaka Lamulungu pa 6 April 2025. Mphepoyi ikuyembekezeka kuchititsa mafunde owopsa otalika mita imodzi (1 metre).
Instructions
1. Tipewe kugwiritsa ntchito ngalawa zing'onozing'ono.
2. Tipewe kusambira panthawiyi.
3. Tisalole ana kusewera pafupi ndi nyanja