Mphepo ya Mwera pa Nyanja
Alert Severity:
Extreme
Severe
Moderate
Minor
Mphepo ya Mwera pa Nyanja
Expired: Strong Mwera winds
Yellow severity
Language:
en
Category:
Met
Urgency:
Expected
Severity:
Moderate
Certainty:
Likely
Time period
-
Issued Fri 14 Mar 2025 12:06
-
Effective: Fri 14 Mar 2025 13:00
-
Onset: Sun 16 Mar 2025 12:01
-
Expires: Tue 18 Mar 2025 12:01
Area
Lake Malawi, Lake Chilwa, Lake Malombe
Event Description
Mphepo ya mphamvu ya Mwera ikuyembekezeka kuomba pa nyanja zathu kuphatikizapo pa nyanja ya Malawi, ya Chilwa ndi ya Malombe.
Instructions
1. Tipewe kugwiritsa ntchito ngalawa zing'onozing'ono.
2. Tipewe kusambira panthawiyi
3. Tisalole ana kusewera pafupi ndi nyanja