Mphepo ya Mwera pa nyanja ya Malawi ndi pa nyanja zina
Alert Severity:
Extreme
Severe
Moderate
Minor
Mphepo ya Mwera pa Nyanja zathu
Expired: Mwera winds
Orange severity
Language:
en
Category:
Met
Urgency:
Future
Severity:
Severe
Certainty:
Likely
Time period
-
Issued Fri 09 May 2025 13:06
-
Effective: Fri 09 May 2025 14:00
-
Onset: Mon 12 May 2025 12:00
-
Expires: Thu 15 May 2025 20:00
Area
Nyanja za Malawi, Chilwa, Malombe
Event Description
Mphepo ya mphamvu ya Mwera ya liwiro la 50km/h ikuyembekezeka kuomba pa nyanja zathu kuphatikizapo pa nyanja ya Malawi, ya Chilwa ndi ya Malombe kuyambira Lolemba pa 12 May 2025 mpaka Lachinayi pa 15 May 2025. Mphepoyi ikuyembekezeka kudzachititsa mafunde owopsa otalika mamita awiri (2 metre).
Instructions
1. Tipewe kugwiritsa ntchito ngalawa zing'onozing'ono.
2. Tipewe kusambira panthawiyi.
3. Tisalole ana kusewera pafupi ndi nyanja