Madzi Osefukira Mwadzidzidzi ku Nyanja
Alert Severity:
Extreme
Severe
Moderate
Minor
Madzi Osefukira Mwadzidzidzi M'mbali Mwa Nyanja Ya Malawi
Expired: Flood
Orange severity
Language:
en
Category:
Met
Urgency:
Future
Severity:
Severe
Certainty:
Likely
Time period
-
Issued Thu 17 Apr 2025 16:17
-
Effective: Thu 17 Apr 2025 17:00
-
Onset: Fri 18 Apr 2025 06:00
-
Expires: Sun 20 Apr 2025 14:00
Area
Karonga, Nkhatabay
Event Description
Mvula ya mphamvu yomwe ikuyembekezeka kugwa m'madera ena am'chigawo cha kumpoto komanso am'mphepete mwa nyanja ingachititse madzi kusefukira mwadzidzidzi makamaka ku Nkhatabay, Karonga.
Instructions
1. Tikhale tcheru
2. Tithawire kumtunda pakakhala chiopsezo cha kusefukira kwa madzi mwadzidzidzi
3. Tisaoloke madzi osefukira
4. Tisalole ana kusewera pafupi ndi mitsinje, madamu kapena mungalande zodutsa madzi.
5. Tikonze ndi kusamalira ngalande zodutsamo madzi