Kuzizira M'madera okwera ndi Apakati
Alert Severity:
Extreme
Severe
Moderate
Minor
Kuzizira M'madera okwera ndi Apakati
Expired: Wind
Minor severity
Language:
en
Category:
Met
Urgency:
Future
Severity:
Minor
Certainty:
Possible
Time period
-
Issued Fri 14 Mar 2025 19:55
-
Effective: Fri 14 Mar 2025 19:55
-
Onset: Fri 14 Mar 2025 21:00
-
Expires: Wed 19 Mar 2025 19:54
Area
Madera okwera ndi am'chigawo chapakati.
Event Description
Tikuyembekezera nyengo yozizira m'madera okwera komanso am'chigawo chapakati kamba ka mphepo yozizira komanso ya chinyontho yochokera kumwera cha kumvuma.
Instructions
1. Tivale za mphepo.
2. Anthu omwe ali ndi vuto la mphumu akuyenera kusamalitsa