Nyengo msabata ikubwerayi 8-14 Dec 2025

Weekly Weather Update

NYENGO M’SABATA IKUBWERAYI

Nyengo ya mitambo ndi yotentha komanso ya mvula ikuyembekezereka kupitilira m’madera ambiri. Mvulayi ikuyembekezereka kugwa yamphamvu m’madera ena maka a m’phepete mwa nyanja ya Malawi.