Nyengo msabata ikubwerayi 17- 23 Feb 2025

Weekly Weather Update

Sabatayi ikuyembekezeka kukhala ya mvula m’madera ochuluka kamba ka dera lodzetsa mvula la ITCZ. Chiopsezo cha kusefukira kwa madzi mwadzidzidzi chikhalanso chokwera m’madera omwe madzi amasefukira kawirikawiri.