Weekly Weather Update 18-24 March 2024

During the period from Monday 18th to Sunday 24th March 2024 expect windy and partly cloudy to cloudy conditions with localized heavy thunderstorms and rain mainly over northern and some central areas while a gradual reduction in rainfall activities is expected over the south.

This is due to the inflow of unstable easterly airmass which at times are expected to converge with south easterlies. Mwera winds are expected occasionally over our water bodies

Kuyambira mawa pa 18 mpaka lamulungu pa 24 March 2024, tiyembekezere nyengo ya mphepo ndi ya mitambo komanso ya mvula yamabingu yomwe pena idzibwera yamphamvu m’madera akumpoto ndi madera ena am’chigawo chapakati pomwe m’madera akumwera mvula idzigwa yapatalipatali. Izi zili chonchi kamba ka mphepo zochokera kumvuma zomwe pena zikhale zikukumana ndi mphepo zochokera kumwera chakumvuma. Mphepo ya Mwera ikhala ikuomba nthawi zina m’sabatayi.