Ulosi wa Nkhotakota wa Dzinja la 2025-2026

None Ulosi wa Mvula mu Dzinja la 2025-2026

Boma la Nkhotakota likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuposera apo munyengo ya dzinja ya 2025/2026.