Ulosi wa Nkhatabay wa Dzinja la 2025-2026

None Ulosi wa Mvula mu Dzinja la 2025-2026

Boma la Nkhatabay likuyembekezera kulandira mvula ya mlingo wokhadzikika kapena kuposerapo ngakhale pali kuthekera kwakukulu koti mvula yochepera mlingo wokhadzikika itha kudzagwa mu November 2025, komanso February 2026.