Ulosi wa Blantyre wa Dzinja la 2025-2026

None Ulosi wa Mvula mu Dzinja la 2025-2026

Boma la Blantyre likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo okhazakika kapena kupyolera apo kuchoka mwezi wa October mp.aka April 2026.palinso kuthekera kwa mlingo okhazikika komanso kuchepera mu miyezi ya November ndi February.