Ulosi wa Dzinja la 2025-2026

Ulosi wa dzinja la 2025-2026 umene ukuunikira ammene mvula igwere mmaboma onse a Malawi. Ulosiwu ukupereka upangili omwe uthandize onse ogwilitsa ntchito ulosiwu kukonzekera ziopysezo zonse zobwera ndi nyengo ya dzinja limeneli

Browse Product Updates

Filter by Year
Filter by Month
Showing 29 results
Ulosi wa Chiradzulu wa Dzinja la 2025-2026
Mvula ya mulingo okhazikika komanso kuposera apo ikuyembekezereka m’boma la Chiradzulu makamaka mmadera akumpoto kwa bomali
Oct. 1, 2025 - April 30, 2026
Read More
Ulosi wa Chitipa wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Chitipa likuyembekezera kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena kuchepera apo mu dzinja la 2025/2026
Oct. 1, 2025 - April 30, 2026
Read More
Ulosi wa Phalombe wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Phalombe likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena woposera apo mu nyengo ya mvula ya 2025/2026.
Oct. 1, 2025 - April 30, 2026
Read More
Ulosi wa Balaka wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Balaka likuyembekeza kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena wocheperapo mu nyengo ya dzinja ya 2025/2026.
Oct. 1, 2025 - April 30, 2026
Read More
Ulosi wa Blantyre wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Blantyre likuyembekezeka kulandira mvula ya mlingo okhazakika kapena kupyolera apo kuchoka mwezi wa October mp.aka April 2026.palinso kuthekera kwa ml…
Oct. 1, 2025 - April 30, 2026
Read More
Ulosi wa Chikwawa wa Dzinja la 2025-2026
Boma la Chikwawa likuyembekeza kulandira mvula ya mlingo wokhazikika kapena yoposera apo mu nyengo ya dzinja la 2025/2026
Oct. 1, 2025 - April 30, 2026
Read More