Nyengo msabata ikubwerayi 21- 27 Oct 2024

Weekly Weather Update

Kukhala kwa nyengo yopanda mvula m'madera ambiri. Koma pali kuthekera kwa mvula yowaza yamabingu m’madera ochepa am’chigawo cha kumpoto ndi okwera am’chigawo cha ku m’mwera.