Tiyembekezere nyengo yamitambo yapatali patali komanso yotentha msabatayi.
🌧️Koma pakati pa lachiwiri masana pa 15 October 2024 mpaka lachinayi pa 17 October 2024, tiyembekezere nyengo ya mphepo, yamitambo komanso mvula ya mabingu m’madera ena.
⚠️🌊Mphepo ya Mwera zikuyembekezereka kuomba mwamphanvu pa nyanja ya Malawi ndi nyanja kuyambira lachiwiri masana pa 15 October 2024 mpakana lachinayi pa 17 October 2024.