Weekly Weather Update

The Malawi Department of Climate Change and Meteorological Services (DCCMS) offers a weekly weather forecast, providing citizens with reliable and up-to-date weather predictions. This essential service helps in planning agricultural, economic, and daily activities, enhancing resilience against weather-related challenges.

Browse Product Updates

Filter by Year
Filter by Month
Showing 30 results
Nyengo msabata ikubwerayi 9 - 15 Sept 2024

Mawa lolemba pa 9 September, 2024, tiyembekezere nyengo ya mphepo, yamitambo yapatali patali komanso yotentha. Izi ndi kamba ka mpweya ofunda ochokera kumvuma.

Koma kuyambira Lachiwiri pa 10 September, mpaka lachinayi pa 12 September, 2024 …

Sept. 9, 2024
Read More
Weekly Weather Update 9- 15 Sept 2024

On Monday, the 9th, expect windy, partly cloudy, and hot to very hot conditions to persist as a warm easterly air mass remains in charge.

From Tuesday, September 10th, through Thursday, September 12th, cloudy conditions …

Sept. 9, 2024
Read More
Nyengo msabata ikubwerayi 2 Sept - 8 Sept 2024

Kuyambira pa Lolemba pa 2 mpaka Lachitatu pa 4 September, 2024 tiyembekezere nyengo Chiperoni kupitilira, yomwe ndi nyengo yamphepo, yozizira ndi mitambo yochuluka komanso mvula yowaza ndi yamawawa komanso chifunga. Pa Nyanja ya Malawi, Chilwa …

Sept. 2, 2024
Read More
Weekly Weather Update 2 Sept - 8 Sept 2024

From Monday, September 2nd, to Wednesday, September 4th, 2024, expect Chiperoni weather to persist, featuring windy, chilly, and overcast conditions, along with light to moderate rain and occasional drizzles, as well as fog patches in …

Sept. 2, 2024
Read More
Nyengo msabata ikubwerayi 26 Aug- 1 Sept 2024

Kuchokera mawa Lolemba pa 26 August 2024 mpaka lachinayi pa 29 August 2024, tiyembekezere nyengo ya mphepo, yamitambo yapatali patali komanso yotentha. Izi ndi kamba ka mpweya ofunda ochokera kumvuma. Koma pomafika madzulo a lachinayi …

Aug. 26, 2024
Read More
Weekly Weather Update 26 Aug- 1 Sept 2024

From Monday, August 26, 2024, to Thursday, August 29, 2024, anticipate windy and partly cloudy weather, with a slight increase in daytime temperatures due to a warm easterly air mass. Beginning Thursday night, August 29, …

Aug. 26, 2024
Read More